Goddy Zambia ft. Macky 2 – Inu Mayi (Official Music Video)

Watch: Goddy Zambia ft Macky 2 - Inu Mayi Video plus Lyrics

Watch: Goddy Zambia ft. Macky 2 – Inu Mayi (Official Music Video)

Goddy Zambia pops up with Macky 2 to deliver the official music video for “Inu Mayi“. Watch: Goddy Zambia ft Macky 2 – Inu Mayi Video plus Lyrics

The new track is taken off his debut studio album “Underrated“.

INU MAYI LYRICS

Inu mayi Kodi mulikumva? ah
Ndingaseke njila Zina koma kunsi ndima sowa Inu
Inu mayi Kodi mukumbukira
Kuti muli ndi Ana mwina munati iwalako
(Inu mayi ,Inu mama kodziko la amalemu uko
Ah ah ah ah inu mayi mugone mu mtendere Inu mama)

VERSE (Goddy)

Kodi mumadya zichani
Kuvala zichani
Kodi nyumba mukhalamo yo Anamanga ndani
Pomwe munafa anakulandilani ndi ndani
Mafunso ndi wambiri pa tisakulise nkhani
Leka ndi kambe ndi yesu ambuye wanga ndinu
Munawadziwa mayi anga asanakhale malemu
Mwina anali muntu ochimwa pa maso panu
Koma kumulanda moyo chinapweteketsa khamu
Kodi munalowa m’jerusalema ?
Mwina munalowako kugahena
Kodi munaonana namalenga
Mwinanu munango werudzika
Munali ndi Ana achichepere ×2
(kudziko munasiya mayi anga?

CHORUS:

Inu mayi Kodi mulikumva ?ah
Ndingaseke njila Zina koma kunsi ndima sowa Inu
Inu mayi Kodi mukumbukira
Kuti muli ndi Ana mwina munati iwalako
(Inu mayi ,Inu mama kodziko la amalemu uko
Ah ah ah ah inu mayi mugone mu mtendere Inu mama)

VERSE : (Macky 2)

Uko kumwamba kwemulili mulungu amisunge,
Apitilize chingiliza devil asanitunke
Ma letter nimamilembela ninshi siyana fike
Ndaba mafunso ninafunsa neo simunayanke
Nikali funo ziba why munanisiya so?
Tinaluvyanya chani ndaba we reap what we sow?
They say celebrate life when somebody dies,
but when we think of you everybody cries
Dear mama! Dear mama! I can’t wait for the day yene tizakakumana.
They told me limba mwamuna samalila,
but chikonko mutima chaugwililila.
Everything I have is all because of you,
so it’s only right I sing this song for you,
and if all this money can’t even bring me joy
then at least let me be a Mama’s boy.

Churned out by Eazy The Producer (Eazy Onafa).
Music Video Directed By: The Epic Director Chichi Ice (Tip Tronic Media Arts) & Director Blue

A Favour Music Presentation.
Executive Producer: Henry Ngosa Mwape (HNM)

Experience it below:

DOWNLOAD AUDIO

NEW VIDEOS |

| ZAMBIAN FACE